Bukuli ndi limodzi mwa zinchito za bungwe la FANSER. FANSER
inakhazikitsidwa ndi unduna wa mgwirizano wa za chuma ndi
chitukuko wa dziko la Germany (BMZ) kukhala ngati ganizo limodzi
lapadera lochedwa DZIKO LIMODZI – Lopanda Njala, lomwe
cholinga chake ndi kugwebana ndi bvuto la njala ndi kuchepekera
kwa chakudya mthupi. Chigawo cha GIZ chinapatsidwa mphamvu
kuti chiyendetse ndondomeko iyi pa dziko lonse.olor sit amet, consectetur adipiscing elit. Ut elit tellus, luctus nec ullamcorper mattis, pulvinar dapibus leo. Download here